CHIVUMBULUTSO 1 : 7
Taonani, adza ndi mitambo; ndipo diso lililonse lidzampenya Iye, iwonso amene anampyoza; ndipo mafuko onse a padziko adzamlira Iye. Terotu.Amen.
# This channel has been created to help those who are far from our braches to have a taste of the word of God. Some of us are in university's, others in areas far away from church or abroad so with this channel we bring the church to you!